Aefeso 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mogwirizana ndi iye,+ inunso mukumangidwa pamodzi kukhala malo oti Mulungu akhalemo mwa mzimu.+