Yeremiya 50:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzafunsira njira yopita ku Ziyoni nkhope zawo zitayang’ana kumeneko.+ Iwo adzanena kuti, ‘Bwerani, tiyeni tidziphatike kwa Yehova mwa kuchita pangano lokhalapo mpaka kalekale limene silidzaiwalika.’+ Machitidwe 10:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+
5 Iwo adzafunsira njira yopita ku Ziyoni nkhope zawo zitayang’ana kumeneko.+ Iwo adzanena kuti, ‘Bwerani, tiyeni tidziphatike kwa Yehova mwa kuchita pangano lokhalapo mpaka kalekale limene silidzaiwalika.’+
45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+