Luka 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tsopano, Ambuye Wamkulu Koposa, mukulola kapolo wanu kupita mu mtendere+ malinga ndi zimene inu munanena.
29 “Tsopano, Ambuye Wamkulu Koposa, mukulola kapolo wanu kupita mu mtendere+ malinga ndi zimene inu munanena.