Malaki 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Koma inu amene mukuopa dzina langa, dzuwa la chilungamo lidzakuwalirani+ ndipo m’mapiko mwake mudzakhala mphamvu yochiritsa.+ Inu mudzanyamuka ndi kudumphadumpha ngati ana a ng’ombe amphongo onenepa.”+
2 “Koma inu amene mukuopa dzina langa, dzuwa la chilungamo lidzakuwalirani+ ndipo m’mapiko mwake mudzakhala mphamvu yochiritsa.+ Inu mudzanyamuka ndi kudumphadumpha ngati ana a ng’ombe amphongo onenepa.”+