Salimo 85:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chilungamo chidzayenda pamaso pake,+Ndipo chidzapanga njira yotsatira mapazi a Mulungu.+ Machitidwe 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+