Hagai 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa makamu. “‘Ndipo ndidzakhazikitsa mtendere pamalo awa,’+ watero Yehova wa makamu.”
9 “‘Ulemerero wa nyumba yatsopanoyi udzakhala waukulu kuposa wa nyumba yoyamba ija,’+ watero Yehova wa makamu. “‘Ndipo ndidzakhazikitsa mtendere pamalo awa,’+ watero Yehova wa makamu.”