Zekariya 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yuda nayenso adzamenya nkhondo mothandizana ndi Yerusalemu, ndipo adzasonkhanitsa chuma cha anthu a mitundu yonse yowazungulira. Adzasonkhanitsa golide, siliva ndi zovala zambirimbiri.+
14 Yuda nayenso adzamenya nkhondo mothandizana ndi Yerusalemu, ndipo adzasonkhanitsa chuma cha anthu a mitundu yonse yowazungulira. Adzasonkhanitsa golide, siliva ndi zovala zambirimbiri.+