2 Mafumu 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’chaka cha 52 cha Azariya mfumu ya Yuda, Peka+ mwana wa Remaliya+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 20.
27 M’chaka cha 52 cha Azariya mfumu ya Yuda, Peka+ mwana wa Remaliya+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 20.