Yesaya 54:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova anakuitana ngati kuti unali mkazi wosiyidwa mpaka kalekale ndi wopwetekedwa mumtima,+ ndiponso ngati mkazi wa paunyamata+ amene kenako anadzasiyidwa,”+ watero Mulungu wako.
6 Yehova anakuitana ngati kuti unali mkazi wosiyidwa mpaka kalekale ndi wopwetekedwa mumtima,+ ndiponso ngati mkazi wa paunyamata+ amene kenako anadzasiyidwa,”+ watero Mulungu wako.