Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+ Yesaya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tulukani m’Babulo anthu inu!+ Thawani m’manja mwa Akasidi.+ Nenani zimenezi ndi mfuu yachisangalalo kuti zimveke.+ Zineneni mokuwa mpaka zimveke kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+
3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+
20 Tulukani m’Babulo anthu inu!+ Thawani m’manja mwa Akasidi.+ Nenani zimenezi ndi mfuu yachisangalalo kuti zimveke.+ Zineneni mokuwa mpaka zimveke kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+