Yeremiya 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima, ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+
5 Ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima, ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+