Numeri 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aliyense amene wakhudza mtembo wa munthu amene waphedwa ndi lupanga,+ kapena mtembo uliwonse, kapenanso fupa la munthu,+ ngakhalenso manda a munthu, akhale wodetsedwa masiku 7. Deuteronomo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kapena wolodza* ena,+ aliyense wofunsira kwa wolankhula ndi mizimu,+ wolosera zam’tsogolo+ kapena aliyense wofunsira kwa akufa.+
16 Aliyense amene wakhudza mtembo wa munthu amene waphedwa ndi lupanga,+ kapena mtembo uliwonse, kapenanso fupa la munthu,+ ngakhalenso manda a munthu, akhale wodetsedwa masiku 7.
11 kapena wolodza* ena,+ aliyense wofunsira kwa wolankhula ndi mizimu,+ wolosera zam’tsogolo+ kapena aliyense wofunsira kwa akufa.+