Levitiko 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “‘Koma pakati pa nyama zimene zimabzikula ndi zimene zili ndi ziboda zogawanika, izi zokha musadye: Ngamila, chifukwa imabzikula koma ziboda zake n’zosagawanika. Nyama imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu.+ Deuteronomo 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Musadye chinthu chilichonse chonyansa.+
4 “‘Koma pakati pa nyama zimene zimabzikula ndi zimene zili ndi ziboda zogawanika, izi zokha musadye: Ngamila, chifukwa imabzikula koma ziboda zake n’zosagawanika. Nyama imeneyi ndi yodetsedwa kwa inu.+