Ezekieli 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Uwauzenso kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga ana a Isiraeli kuchokera pakati pa mitundu ina ya anthu kumene anapita. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera m’mayiko owazungulira ndipo ndidzawabweretsa m’dziko lawo.+ Aroma 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero, pa nthawi ino alipo ena ochepa+ amene anasankhidwa+ mwa kukoma mtima kwakukulu.
21 “Uwauzenso kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga ana a Isiraeli kuchokera pakati pa mitundu ina ya anthu kumene anapita. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera m’mayiko owazungulira ndipo ndidzawabweretsa m’dziko lawo.+