Chivumbulutso 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye adzapukuta misozi+ yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira,+ kapena kubuula, ngakhale kupweteka. Zakalezo zapita.”+
4 Iye adzapukuta misozi+ yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira,+ kapena kubuula, ngakhale kupweteka. Zakalezo zapita.”+