Salimo 45:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mangirira lupanga lako+ m’chiuno mwako wamphamvu iwe,+Limodzi ndi ulemu ndiponso ulemerero wako.+ Yohane 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+
18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+