2 Mafumu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo. Amosi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Komanso ine ndinakupatsani njala*+ m’mizinda yanu yonse ndipo munali kusowa chakudya m’malo anu onse okhala,+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova. Amosi 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesetsani kuyandikira kwa Yehova, inu a m’nyumba ya Yosefe,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndiponso kuti Mulungu asakuyakireni ngati moto.+ Chitani zimenezi kuti motowo usakunyeketseni chifukwa ku Beteli sikungapezeke munthu wouzimitsa.+
14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo.
6 “‘Komanso ine ndinakupatsani njala*+ m’mizinda yanu yonse ndipo munali kusowa chakudya m’malo anu onse okhala,+ koma simunabwerere kwa ine,’+ watero Yehova.
6 Yesetsani kuyandikira kwa Yehova, inu a m’nyumba ya Yosefe,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndiponso kuti Mulungu asakuyakireni ngati moto.+ Chitani zimenezi kuti motowo usakunyeketseni chifukwa ku Beteli sikungapezeke munthu wouzimitsa.+