Levitiko 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Zikondwerero+ za Yehova zimene muyenera kulengeza+ ndiyo misonkhano yopatulika. Izi ndi zikondwerero zanga: Salimo 81:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa tsiku lokhala mwezi, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+Pa tsiku looneka mwezi wathunthu, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, loimba pa tsiku la chikondwerero.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Zikondwerero+ za Yehova zimene muyenera kulengeza+ ndiyo misonkhano yopatulika. Izi ndi zikondwerero zanga:
3 Pa tsiku lokhala mwezi, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa.+Pa tsiku looneka mwezi wathunthu, imbani lipenga la nyanga ya nkhosa, loimba pa tsiku la chikondwerero.+