Yuda 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pamene Mikayeli+ mkulu wa angelo+ anasemphana maganizo+ ndi Mdyerekezi ndipo anakangana naye za mtembo wa Mose,+ sanayese n’komwe kumuweruza ndi mawu onyoza,+ m’malomwake anati: “Yehova akudzudzule.”+
9 Koma pamene Mikayeli+ mkulu wa angelo+ anasemphana maganizo+ ndi Mdyerekezi ndipo anakangana naye za mtembo wa Mose,+ sanayese n’komwe kumuweruza ndi mawu onyoza,+ m’malomwake anati: “Yehova akudzudzule.”+