Yeremiya 48:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 N’chifukwa chake Mowabu ndidzamukuwira, ndipo ndidzafuulira Mowabu yense.+ Anthu adzalirira amuna a ku Kiri-haresi.+
31 N’chifukwa chake Mowabu ndidzamukuwira, ndipo ndidzafuulira Mowabu yense.+ Anthu adzalirira amuna a ku Kiri-haresi.+