Yesaya 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aliyense adzakhala ngati malo obisalirapo mphepo ndi malo ousapo mvula yamkuntho,+ ngati mitsinje yamadzi m’dziko lopanda madzi,+ ndiponso ngati mthunzi wa thanthwe lalikulu m’dziko louma.+
2 Aliyense adzakhala ngati malo obisalirapo mphepo ndi malo ousapo mvula yamkuntho,+ ngati mitsinje yamadzi m’dziko lopanda madzi,+ ndiponso ngati mthunzi wa thanthwe lalikulu m’dziko louma.+