Deuteronomo 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova Mulungu wako adzachititsanso mantha mitima yawo+ kufikira onse otsala+ ndiponso amene anali kubisala pamaso pako atawonongedwa. Yoswa 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Titangomva zimenezi, mitima yathu inayamba kusungunuka ndi mantha,+ ndipo mpaka pano palibe aliyense amene akulimba mtima, chifukwa choopa inu.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanu ndiye Mulungu wa kumwamba ndi padziko lapansi.+
20 Yehova Mulungu wako adzachititsanso mantha mitima yawo+ kufikira onse otsala+ ndiponso amene anali kubisala pamaso pako atawonongedwa.
11 Titangomva zimenezi, mitima yathu inayamba kusungunuka ndi mantha,+ ndipo mpaka pano palibe aliyense amene akulimba mtima, chifukwa choopa inu.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanu ndiye Mulungu wa kumwamba ndi padziko lapansi.+