Yobu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi ungazindikire zinthu zozama za Mulungu,+Kapena kodi ungadziwe mapeto a kukula kwa Wamphamvuyonse? Aroma 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?
7 Kodi ungazindikire zinthu zozama za Mulungu,+Kapena kodi ungadziwe mapeto a kukula kwa Wamphamvuyonse?
33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?