Yesaya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu wokalamba ndi wolemekezeka kwambiri ndiye mutu,+ ndipo mneneri wopereka malangizo abodza ndiye mchira.+
15 Munthu wokalamba ndi wolemekezeka kwambiri ndiye mutu,+ ndipo mneneri wopereka malangizo abodza ndiye mchira.+