Deuteronomo 28:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo udzakhala chodabwitsa,+ adzakupekera mwambi+ ndi kukutonza pakati pa mitundu yonse ya anthu amene Yehova adzakupititsako. Salimo 44:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwatisandutsa mwambi pakati pa anthu a mitundu ina,+Mwatisandutsa anthu amene anthu a mitundu inawo akuwapukusira mitu.+
37 Pamenepo udzakhala chodabwitsa,+ adzakupekera mwambi+ ndi kukutonza pakati pa mitundu yonse ya anthu amene Yehova adzakupititsako.
14 Mwatisandutsa mwambi pakati pa anthu a mitundu ina,+Mwatisandutsa anthu amene anthu a mitundu inawo akuwapukusira mitu.+