Machitidwe 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho anawagwira ndi kuwasunga m’ndende mpaka tsiku lotsatira,+ chifukwa anali kale madzulo.