Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.] 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]
23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.