Ezekieli 33:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Koma iwe mwana wa munthu, anthu a mtundu wako akukambirana za iwe m’mbali mwa mpanda ndi m’makomo a nyumba.+ Aliyense akuuza m’bale wake kuti, ‘Bwerani mudzamve mawu a Yehova.’+
30 “Koma iwe mwana wa munthu, anthu a mtundu wako akukambirana za iwe m’mbali mwa mpanda ndi m’makomo a nyumba.+ Aliyense akuuza m’bale wake kuti, ‘Bwerani mudzamve mawu a Yehova.’+