Yeremiya 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndidzakuimbani mlandu+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zanu,’+ watero Yehova. ‘Ndidzayatsanso moto m’nkhalango za mzindawu,+ moti udzanyeketsa zinthu zonse zouzungulira.’”+ Zekariya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Iwe Lebanoni,+ tsegula zitseko zako kuti moto utenthe mitengo yako ya mkungudza.+
14 ndidzakuimbani mlandu+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zanu,’+ watero Yehova. ‘Ndidzayatsanso moto m’nkhalango za mzindawu,+ moti udzanyeketsa zinthu zonse zouzungulira.’”+