2 Mafumu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero iye anatengera Yehoyakini+ ku Babulo.+ Anatenga ku Yerusalemu mayi a mfumuyo,+ akazi ake, nduna za panyumba yake,+ ndi akuluakulu a m’dzikolo, n’kuwapititsa ku Babulo. 1 Mbiri 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana amene Yekoniya anabereka ali mkaidi anali Salatiyeli,+
15 Chotero iye anatengera Yehoyakini+ ku Babulo.+ Anatenga ku Yerusalemu mayi a mfumuyo,+ akazi ake, nduna za panyumba yake,+ ndi akuluakulu a m’dzikolo, n’kuwapititsa ku Babulo.