Yeremiya 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Yehova wanena kuti: “Funsafunsani pakati pa mitundu ya anthu. Ndani anamvapo zoterezi? Namwali wa Isiraeli wachita chinthu choopsa mopyola malire.+
13 Choncho Yehova wanena kuti: “Funsafunsani pakati pa mitundu ya anthu. Ndani anamvapo zoterezi? Namwali wa Isiraeli wachita chinthu choopsa mopyola malire.+