Deuteronomo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 mwamuna woyamba amene anam’chotsa uja sadzaloledwa kum’tenganso kuti akhale mkazi wake pambuyo poti waipitsidwa.+ Kuchita zimenezo n’konyansa pamaso pa Yehova, chotero usachimwitse dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa monga cholowa.
4 mwamuna woyamba amene anam’chotsa uja sadzaloledwa kum’tenganso kuti akhale mkazi wake pambuyo poti waipitsidwa.+ Kuchita zimenezo n’konyansa pamaso pa Yehova, chotero usachimwitse dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa monga cholowa.