Yeremiya 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Unganene bwanji kuti, ‘Sindinadziipitse.+ Sindinatsatire mafano a Baala’?+ Ganizira bwinobwino njira yako m’chigwa.+ Onetsetsa zimene wachita. Wakhala ngati ngamila yaing’ono yaikazi imene ikungothamangira uku ndi uku.
23 Unganene bwanji kuti, ‘Sindinadziipitse.+ Sindinatsatire mafano a Baala’?+ Ganizira bwinobwino njira yako m’chigwa.+ Onetsetsa zimene wachita. Wakhala ngati ngamila yaing’ono yaikazi imene ikungothamangira uku ndi uku.