Yeremiya 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Ndidzaika magoli achitsulo pamakosi a mitundu ya anthu yonseyi kuti atumikire Nebukadinezara mfumu ya Babulo,+ ndipo ndikunenetsa kuti adzamutumikiradi.+ Nebukadinezara ndidzamupatsanso ngakhale nyama zakutchire.”’”+ Danieli 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inuyo mfumu, mfumu ya mafumu, inu amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu, ndi ulemerero,
14 Pakuti Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Ndidzaika magoli achitsulo pamakosi a mitundu ya anthu yonseyi kuti atumikire Nebukadinezara mfumu ya Babulo,+ ndipo ndikunenetsa kuti adzamutumikiradi.+ Nebukadinezara ndidzamupatsanso ngakhale nyama zakutchire.”’”+
37 Inuyo mfumu, mfumu ya mafumu, inu amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu, ndi ulemerero,