Deuteronomo 28:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Pamenepo udzadya chipatso cha mimba yako, mnofu wa ana ako aamuna ndi ana ako aakazi,+ amene Yehova Mulungu wako wakupatsa, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani ako adzakupanikiza nazo. Ezekieli 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Zidzateronso ndikadzabweretsa ziweruzo zanga zinayi izi zowononga:+ lupanga, njala, zilombo zolusa zakutchire ndi mliri.+ Ndidzatumiza zimenezi mu Yerusalemu kuti zikaphemo anthu ndi ziweto.+
53 Pamenepo udzadya chipatso cha mimba yako, mnofu wa ana ako aamuna ndi ana ako aakazi,+ amene Yehova Mulungu wako wakupatsa, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani ako adzakupanikiza nazo.
21 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Zidzateronso ndikadzabweretsa ziweruzo zanga zinayi izi zowononga:+ lupanga, njala, zilombo zolusa zakutchire ndi mliri.+ Ndidzatumiza zimenezi mu Yerusalemu kuti zikaphemo anthu ndi ziweto.+