Miyambo 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choka pamaso pa munthu wopusa,+ chifukwa supeza nzeru m’mawu otuluka pakamwa pake.+ Miyambo 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usayankhe aliyense wopusa mogwirizana ndi uchitsiru wake, kuti iweyo usafanane naye.+