Yeremiya 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Uli ndi tsogolo labwino+ ndipo ana ako adzabwerera kudziko lawo,’+ watero Yehova.”