Yeremiya 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Ine sindinawatume,’ watero Yehova, ‘koma iwo akulosera m’dzina langa monama, ndipo mukawamvera ndidzakubalalitsani.+ Inu pamodzi ndi aneneri amene akulosera kwa inuwo mudzatha.’”+
15 “‘Ine sindinawatume,’ watero Yehova, ‘koma iwo akulosera m’dzina langa monama, ndipo mukawamvera ndidzakubalalitsani.+ Inu pamodzi ndi aneneri amene akulosera kwa inuwo mudzatha.’”+