Yeremiya 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Yehova wanena kuti, ‘Ndikukuchotsera moyo wako. Chaka chomwe chino iweyo ufa,+ chifukwa zimene wanenazo ndi kupandukira Yehova kwenikweni.’”+
16 Chotero Yehova wanena kuti, ‘Ndikukuchotsera moyo wako. Chaka chomwe chino iweyo ufa,+ chifukwa zimene wanenazo ndi kupandukira Yehova kwenikweni.’”+