Zekariya 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndikuwaloza mowaopseza,+ ndipo adzatengedwa ndi akapolo awo kuti akhale chuma cha akapolowo.’+ Ndithu, anthu inu mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma.+
9 Ine ndikuwaloza mowaopseza,+ ndipo adzatengedwa ndi akapolo awo kuti akhale chuma cha akapolowo.’+ Ndithu, anthu inu mudzadziwa kuti Yehova wa makamu wandituma.+