Mateyu 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mawu anamveka ku Rama,+ kulira ndi kubuma mofuula. Anali Rakele+ kulirira ana ake ndipo sanamve kumutonthoza, chifukwa ana akewo kunalibenso.”
18 “Mawu anamveka ku Rama,+ kulira ndi kubuma mofuula. Anali Rakele+ kulirira ana ake ndipo sanamve kumutonthoza, chifukwa ana akewo kunalibenso.”