Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wapereka madzi kwa anthu aludzu.+Ndipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+ Yesaya 40:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa,+ ndipo wofooka amam’patsa nyonga zochuluka.+