Salimo 72:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzakuopani nthawi zonse pamene dzuwa likuwala,+Adzakuopani ku mibadwomibadwo pamene mwezi uli kuthambo.+
5 Iwo adzakuopani nthawi zonse pamene dzuwa likuwala,+Adzakuopani ku mibadwomibadwo pamene mwezi uli kuthambo.+