Hoseya 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Kodi ndikuchite chiyani iwe Efuraimu? Nanga iwe Yuda, ndikuchite chiyani?+ Anthu inu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kofanana ndi mitambo ya m’mawa, ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma.
4 “Kodi ndikuchite chiyani iwe Efuraimu? Nanga iwe Yuda, ndikuchite chiyani?+ Anthu inu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kofanana ndi mitambo ya m’mawa, ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma.