Nehemiya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Awa ndi mawu a Nehemiya+ mwana wa Hakaliya. M’mwezi wa Kisilevi,*+ m’chaka cha 20,+ ine ndinali kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.+
1 Awa ndi mawu a Nehemiya+ mwana wa Hakaliya. M’mwezi wa Kisilevi,*+ m’chaka cha 20,+ ine ndinali kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.+