Yeremiya 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muwaphe ndi kusiya mitembo yawo ili paliponse m’dziko la Akasidi.+ Muwasiye mutawabaya m’misewu ya m’dzikolo.+
4 Muwaphe ndi kusiya mitembo yawo ili paliponse m’dziko la Akasidi.+ Muwasiye mutawabaya m’misewu ya m’dzikolo.+