Yeremiya 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwina ukatero Yehova adzamva pempho lawo lakuti awakomere mtima+ ndipo aliyense adzabwerera kusiya njira yake yoipa,+ chifukwa Yehova wanena kuti adzasonyeza anthu awa mkwiyo wake waukulu ndi ukali wake.”+
7 Mwina ukatero Yehova adzamva pempho lawo lakuti awakomere mtima+ ndipo aliyense adzabwerera kusiya njira yake yoipa,+ chifukwa Yehova wanena kuti adzasonyeza anthu awa mkwiyo wake waukulu ndi ukali wake.”+