4 ndipo Zedekiya mfumu ya Yuda sadzapulumuka m’manja mwa Akasidi, pakuti adzaperekedwa ndithu m’manja mwa mfumu ya Babulo moti adzalankhulana ndi kuonana maso ndi maso ndi mfumuyo?”’+
18 Koma ngati simudzadzipereka kwa akalonga a mfumu ya Babulo, ndiye kuti mzinda uno udzaperekedwa m’manja mwa Akasidi ndipo adzautentha.+ Inuyo simudzapulumuka m’manja mwawo.’”+