Yesaya 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Udzu wobiriwirawo wauma. Maluwawo afota.+ Koma mawu a Mulungu wathu adzakhala mpaka kalekale.”+