-
Yeremiya 36:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Pamenepo Yeremiya anatenga mpukutu wina ndi kuupereka kwa Baruki mlembi,+ mwana wa Neriya. Baruki analembamo mawu onse amene Yeremiya anamuuza,+ mawu onse amene anali mumpukutu umene Yehoyakimu mfumu ya Yuda anatentha.+ Mumpukutumo anawonjezeramo mawu ena ambiri ofanana ndi a mumpukutu woyamba uja.
-